Use APKPure App
Get Quran Chichewa old version APK for Android
Corano ya Chichewa offline gratuito.
Corano ya Chichewa/Chinyanja offline ikupezeka tsopano pa internet.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chinyanja/ Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa/Chinyanja.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabic.
Ndipo kwa opanga Da'wa pa masamba a mchezo yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copia e incolla kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Basta fare un lungo clic per copiare e incollare)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.
Last updated on Sep 23, 2020
Added missing Surah
Caricata da
Sandal Raj
È necessario Android
Android 4.4+
Categoria
Segnala
Quran Chichewa
7.2 by Muhammad Golden
Sep 23, 2020