Use APKPure App
Get Quran Chichewa old version APK for Android
Alquran ya Chichewa offline gratis.
Qur'an ya Chichewa/Chinyanja offline ikupezeka tsopano pa internet.
Ili ndi nemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chinyanja/ Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa /Chinyanja.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Dakwah mma media sosial komanso awo omwe sabva Arabic.
Ndipo kwa opanga Da'wa pa masamba a mchezo yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga salin dan tempel kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Cukup klik panjang untuk menyalin dan menempel)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.
Last updated on Sep 23, 2020
Added missing Surah
Diunggah oleh
Sandal Raj
Perlu Android versi
Android 4.4+
Kategori
Laporkan
Quran Chichewa
7.2 by Muhammad Golden
Sep 23, 2020